0	,	Koma nanu azipani atsogoleri
1	,	Musakomedwe n 'kulorif eza
2	,	Pongotengera mwayi
3	,	lnde wolankhula pa wayilesi
4	,	lnde zambiri mwalonjezadi
5	,	Koma ichi dziwani
6	,	Wadzisuletu nsapato samulonjeza
7	,	Ndife 'agocho '
8	,	Ndiye musatilonjeze mwana Zero
9	,	Poti mukadzapanda kutipatsa mawa
10	,	Zanuzo nsapato
11	,	Tidzakulandani
