0	,	Mwachitanji nanga
1	,	Poti 1999 ija yafika
2	,	Munkati tikumvetsani
3	,	Mukubwebwetuka ndi mapulani a chitukuko
4	,	Nanga mwachitanji?
5	,	Suuja munkati kulibe misewu kukhale misewu
6	,	Nanga muvotere yani a Malawi
7	,	Pott 1999 yafika
8	,	Mwachitanji anzanga?
