0	,	Chitukuko chachitikadi
1	,	Chitukuko chake chosaoneka
2	,	Tiyeni tiwone za chitukukochi
3	,	Chitukuko cha Bakili
4	,	Kusowa kwa mankhwala m 'zipatala
5	,	Jcho ndicho chitukuko choyamba
6	,	Kuchedwa kwa malipiro a aphunzitsi
7	,	Chitukuko cha Bakili
8	,	Chitukuko chanji chokhalira kuyendayenda
9	,	Chitukuko chogula ma MP m 'malo mwa chimanga
10	,	Zikakhala zokonza misewu taiwala
11	,	Aah! !chi sichitukuko koma kampeni
12	,	Chitukuko cha Bakili, Uuuu!
13	,	Zinthu zatotanidyee?
