0	,	Kwezani maso a Malawi
1	,	Kukwezera ku tsikulo
2	,	Zamitsani nzeru inu
3	,	Usapite wotere mwayi makosana
4	,	Zidze pano nzatonse nthuni
5	,	Mosasamala anasankha oziyelekera ubwino
6	,	Atilangitsa ife - atipweteka
7	,	Taphedwa mokwana, tamangidwa mokwana
8	,	Ali kuti malume ngati sali kuli chete
9	,	Tisakanganenso za zipani tiyeni tiganize mwakuya
10	,	Papita pokambakamba tsono tisankhe
11	,	Tengani mbali pokonza tsogo/o
12	,	Tsogolo lopatsa chidwi ndinso laufulu
