0	,	Anthuni
1	,	lmvani
2	,	Lero ndafuna ndikuuzeni
3	,	Za m 'nyamata wina
4	,	Yemwe lake dzina, Kalua
5	,	Mnyamatayi
6	,	Omudziwa bwino akuti
7	,	Ake malonda anali
8	,	Ogulitsa chamba
9	,	Ndi mankhwala ena owononga bongo
10	,	Anthuni
11	,	Mosayembekeza
12	,	Lero mnyamatayi
13	,	Akuti tizilemekeza Kamuzu
14	,	Pamene iye ankatukwana yomweyo
15	,	Kamuzu
16	,	Kodi tilakwa
17	,	Tikaganiza kuti mnyamatayi
18	,	Wagulidwa ndi kongeresi
19	,	Kapena kuti amatukwana
20	,	Pa Channel Africa chili boo-boo!
21	,	M'mutu chamba
