0	,	Wopanda ulemu ndipo wosayamika
1	,	Ndifetu a Malawi
2	,	Lathu dziko Ngwazi ndiye walikwezadi
3	,	Yathu miyoyo ndiye watukuladi
4	,	Koma lero kumtoso ndiye tikumtengera
5	,	Monga a njoka maliro m 'malo momthokoza
6	,	Kodi kukhala ndi choncho?
7	,	Tayamba kuluma dzanja
8	,	lotidyetsa, kupanda pabwino!
9	,	chifukwa chati mbee! Sichinapse/
10	,	Ndipo chati thubwi, sichinaoloke
