0,	Nyali yawala
1,	Y awaladi nyali
2,	M'dima wathawa
3,	Tambala walira nayesa kunja kwacha
4,	Kuwala kodabwitsako kwamufikira
5,	Zachisoni iye wakondadi m 'dima
6,	Mwake mumtima mtendere umusowa
7,	Monga mbalame yopanda chisa tulo alisowadi
8,	Monyansidwa ayesayesa kuthimitsa nyaliyo
9,	Wake mdima akutero
10,	Lero ndife afulu enieni
11,	Kukhala sikumeneku anthuni?
12,	Unali kuti nthawi yonseyi?
