,0
0,Kwabwera mwana wodzakhala m’nyumba mwanu?
1,Ukwati wanu watha kapena mwasiyana ndi akazi anu?
2,Munamvetsedwa kuti mwapeleka mimba?
3,Mwasamukira kunyumba yabwinoko?
4,Mwasamukira kunyumba yosakhala bwino?
5,Mwafunsilapo mkazi wina?
6,Munazizwa nazo?
7,Kwabwera anthu ena achikulire odzakhala m’nyumba mwanu?
8,Mwana wanu anamwalira
9, Kumwalira kwa makolo
10,Kumwalira kwa nzanu wapamtima
11, Kumwalira kwa mchimwene/mchemwali wanu
12, Kumwalira kwa munthu wina okhala mnyumba mwanu?
13, Akazi/chibwenzi chanu chasamukila kukakhala kuntchito
14,Umoyo wanu wanthupi wapita patsogolo?
15,Umoyo wanu wanthupi walowa pansi?
16,Mwakumana ndi vuto lochepa chakudya mnyumba?
17,Kodi mwamva mphekesela yoti akazi/chibwenzi chanu akuyenda ndi amuna ena?
18,Kodi kulemela kwathupi lanu kwasika?
19,Kodi kulemela kwathupi la akazi/chibwenzi chanu kwasika?
20,Mkazi/chibwenzi chanu chatisiya/chamwalira?
21,Mwapeza ntchito yabwino
22,Kodi pali wina aliyense mnyumba mwanu yemwe wakhudzidwapo ndi ufiti?
23,Kodi akazi/chibwenzi chanu chidakhudzidwapo ndi ngozi iliyonse?
24,Kodi akazi/chibwenzi chanu chakhala chikudwala?
25,Kodi akazi/chibwenzi chanu apeza ntchito yabwino?
26,"chanu chachoka pantchito, chasinthidwa kapena wapeza ntchito yosakhala bwino"
27,Kodi akazi anu/chibwenzi chanu anapita pachabe?
28,Kodi akazi anu/chibwenzi chanu anataya mimba?
29,Munagonekedwa kuchipatala?
30,Kodi mwakakamizidwa ndi abale anu kuti mukhale ndi ana?
31,Munavulala kapena kuchita ngozi?
32,Munadwalapo malungo?
33,Wakumanako ndi vuto lolipira fizi?
34,Wakumanako ndi vuto kusukulu?
35,ntchito; kapena mwapeza ntchito yosakhala bwino
36,Munakhudzidwapo ndi ufiti?
37,Mwafunsirapo ukwati?
38,Kudwala kwa mwana
39,Kudwala kwa makolo?
40,Kudwala kwa mchimwene kapena mchemwali?
41,Munadalitsa ukwati?
42,Munachita chinkhonswe?
43,Munangotengana/munangolowana?
44,Munadulitsa ntchatho?
