0,"Mongoyelekeza, mwayenda mtunda wautali bwanji kuti mufike kuno?"
1,"Mongoyelekeza, zinakutengelani nthawi yayitali bwanji kuti mufike kuno?"
2,Ndi ndani amene anakupelekezani?
3,Alipo amene anakupelekezani?
4,"Nanga zokhuza inuyo, mbiri yanu?"
5,Kodi ndinu a mtundu wanji?
6,Kodi ndi ziyankhulo ziti zimene mukhonza kuyankhula bwinobwino?
7,Ndi anthu angati kuphatikizapo inuyo amene amagona mnyumba mwanu nthawi zambiri?
8,Ndi ana angati omwe ali ndi zaka zosaposera 15?
9,Ndi angati achikulire ali oposera zaka 64?
10,Ndi angati omwe ali ndi zaka pakati pa 15
11,Munabadwa chaka chanji?
12,Mumakhala mudzi wanji? 
13,Mudzi umenewo uli m'balaka muno?
14,"Kodi umewu ndi mzinda, tauni, Trading Centre kapena ndi mudzi?"
15,Mumatenga nthawi yaitali bwanji kuh muyende kukafika ku Trading Centre imene muli nayo pafupi?
16,Kodi chibadwireni mwakhala mull m'dera limeneli? 
17,Mwakhala nthawi yaitali bwanji kudelalino?
18,Ndi chifukwa chiti chenicheni chomwe munasamukira kudelalino? 
19,Kuyambira pomwe munali zaka zisanu ndimadera ena angati asiyanasiyana amene mwakhalako kwa miyezi itatu kapena kuposera apo?
20,Kodi munalekaza kalasi/fomu iti?
21,Kodi pakali pano muli pa sukulu? 
22,Tsopano tisewela masewela
23, Ndiwelenga manambala ena kwa inu kamodzi kokha
24, Ndidzadikira kwa kanthawi pang'ono kenako ndidzakufunsani kuti mubweleze ma nambalawo
25, Mwakonzeka kuti tiyambe?
26,Nthawi yomaliza imene munabwera kuno munandifotokozera za ana anu
27, Tsopano ndikufunsani za ana amenewa komanso za ana ena amene muli nawo kapena mwakhala nawo
28, Ndikufuna ndi dziwem'ndandanda wa ana onse amene munabereka amoyo
29,Chonde ndiwuzeni dzina/maina a anawa
30,Kodi [DZINA] ndi wamkazi/wammuna?
31,Kodi [DZINA] anabadwa mwezi ndi chaka chiti?
32,Kodi dzina la bambo ake a(dzina) omubeleka ndi ndani?
33,Kodi dzina la bambo ake a(dzina) omubeleka ndi ndani?
34,Kodi bambo ake a(dzina) omubeleka mumakhala nawo nyumba imodzi?
35,"Kodi mwanayu anabadwira kunyumba, kuchipatala, kapena kwina kwake?"
36,Sikelo yake [DZINA] inakwana bwanji atangobadwa?
37,Kodi munalandira mphatso ya ndalama kuchokera ku chipatala nthawi imene munali ndi mimba kapena atabadwa mwanayu?
38,Kodi munalandira mphatso ya ndalama zingati?
39,Kodi munapeleka chindapusa kwa amfumu chifukwa chamimbayi kapena mutabeleka mwanayu?
40,Kodi amfumu anakulipitsani chindapusa chandalama zingati?
41,Ndi chifukwa chani anfumu anakulipitsani chindapusa?
42,Chifukwa chani [DZINA] sakhala ndi inu?
43,Wabwino koposa
44,Bwino kwambiri
45,Bwino
46,Choncho
47,Suli bwino konse
48,Kodi mungasiyanitse motani umoyo wa [DZINA] ndi anthu ena a m’mudzi mwanu omwe akufanana nawo zaka?
49,Uli bwino kwambiri
50,Uli bwino ndithu
51,Siunasinthe
52,Siwuli bwino
53,Siwuli bwino konse
54,"Pa masabata awiri apitawa [DZINA], anadwalapo chifuwa chophatikizana ndi kubanika?"
55,Pa masabata awiri apitawa [DZINA] anatenthapo thupi?
56,Kodi (dzina) alipa sukulu?
57,Kodi (dzina) anayamba sukulu ali ndi zaka zingati?
58,Ndi ana angati onse amene munabelekapo chiyambile kuphatikizilapo omwe anamwalira?
59,Kodi pakali pano ndinu oyembekezera?
60,Ndinu oyembekezera kwa miyezi ingati?
61,"Nthawi zina amayi amakhala oyembekezera ndipo amatha kupita padera, komaso nthawi zina amasankha kuchotsa pathupi"
62," Ndili ndi chidwi ndi nthawi zonse zomwe munazindikira kuti mwakhala oyembekezera zimene simunabeleke mwana wa moyo kuphatikizapo kupita padera kutaya mimba ndi kubeleka mwana wakufa, chonde mungandiuzeko za mimba zimenezi kuchokera chaka cha 2012?"
63,Kupita padera 
64,Kutaya pathupi
65,Ntayo 
66,Funsoli likufunsa za njila zolerera
67," Izi zikhoza kukhala makondomu, mapilitsi, jekeseni, norplant kapena kutseka kwa abambo kapena amai kapena njira ina iri yonse yoteteza kuti musatenge mimba"
68, Mwezi omwe ndinatenga mimba
69,Mafunso angapo otsatilawa ndi okhudza inuyo musanakhale ndi mimba
70,Ndinali ndi cholinga chotenga mimba
71,Ndinkasinthasintha maganizo
72,Ndinalibe cholinga chokhala ndi mimba
73,Ndimafuna kukhala ndi mwana
74,Ndinali ndi maganizo osiyanasiyana pa zokhala ndi mwana
75,Sindimafuna kukhala ndi mwana
76,Kodi mungakonde mutadikira nthawi yaitali bwanji musanabereke mwana wanu woyamba/wotsatira?
77,Pompano/posachedwa pa
78,Pasanathe zaka ziwiri
79,Zaka ziwiri kufikira zitatu
80,Zaka zitatu kufikira zaka zinayi
81,Zaka zinayi kufikira zaka zisanu
82,Zaka zisanu kapena kuposela apo
83,Mulimonse/nthawi ina iliyonse
84,Mwamuna wanu wapeza ntchito yamalipiro abwino ndi yokhazikika
85,Mwapeza ntchito yamalipiro abwino ndi yokhazikika
86,Mwamva mphekesera yoti mwamuna wanu akugonana ndi akazi ena
87,Mwamuna wanu akufuna ana ocheperapo kuposa omwe inu mukufuna
88,Mwana wanu wamng'ono kwambiri akudwala mwakayakaya
89,Muli ndi ana amuna okha okha
90,Muli ndi ana akazi okha okha
91,Mayi anu akudwala mwakayakaya
92,Mayi anu amwalira
93,Mwazindikira kuti muli ndi HIV koma mulibe zizindikiro zilizonse
94,Ndikufuna ndidziwe zochitika m’moyo wanu
95, 
96,"Poganizira zinthu zonse, Kodi ndinu wokhutira bwanji ndi moyo wanu?"
97,"Kodi mukuganiza kuti ndinu okhutitsidwa kwambiri, chimodzimodzi kapena pang'ono poyelekeza ndi anthu ena amene mukufanana nawo zaka a m'mudzi mwanu?"
98,Ndinali okhumudwa
99,Ndimaona ngati bola ndidakangofa
100,Ndinali okwanilitsidwa
101,Pafupipafupi kwambiri 
102,Pafupipafupi
103,Nthawi zina
104,Pafupifupi sizinachitikepo
105,Sizinandichitikilepo 
106,Ndinagokhala ndekha ndekha
107,Ndalephera kuwongolela zinthu zofunika pa moyo wanga
108,Ndimazikhulupilira kuti ndili ndi kuthekera kothana ndi mavuto anga
109,Kodi ndi anthu angati amene mwagonana nawo chiyambire kuchita zogonana?
110,Ndiye mukuti simunagonane ndi wina aliyense?
111,Kodi kuyamba kugonana ndi munthu munagonana naye muli ndi zaka zingati?
112,Kodi mzanuyu ali ndi ana pakali pano?
113,Kodi pakalipano ndiwoyembekezera?
